Bungwe la oyimba la Copy right Society of Malawi (COSOMA) lati mawa lipereka ndalama za nkhaninkhani kwa oyimba m’dziko muno kudzera ku thumba la bungwe...
Mtsogoleri wa mpingo wa Salvation for All Ministries International, Apostle Clifford Kawinga, wapereka K25 million kunyumba yosunga ana amasiye ya Home of Hope Orphanage m’boma...
Khonsolo ya mnzinda wa Lilongwe yati ndi yodzipereka pa ntchito yolimbikitsa bata ndi mtendere m’dziko muno. Wachiwiri kwa mfumu ya mnzinda wa Lilongwe, a Ruth...
Mkulu woona za zamaphunziro a zachuma ku Old Mutual a Bernard Chiluzi ati anthu ambiri amene akukhuzidwa ndi mchitidwe odzipha m’dziko muno akuchita izi kaamba...
Mwini wake wa kampani ya J.S Fitness ku Lilongwe, a Clement Udedi ati ndikofunika kuti aliyense atengepo gawo pothana ndi matenda a cancer ya m’mawere....
Cooperative ya Salima Cane Growers yati pofika pa 30 September chaka chino, inakwanitsa kupeza ndalama zoposa K620 million kuchokera ku ulimi wa nzimbe itagulitsa nzimbe...
Apolisi ku Lilongwe amanga Wyson Misoya ndi mkazi wake Gloria onse azaka 32 powaganizira kuti aba mwana wamasiku awiri pa chipatala cha Kamuzu Central ku...
Chipatala cha South Lunzu m’boma la Blantyre chakonza ulendo wa ndawala mwezi wa mawa pofuna kupeza thandizo la ndalama zokwana K70 million zimene akufuna kuti...