Bungwe la Malawi Electoral Commission (MEC) lati lionjezera masiku mu kalembera wachisankho m’gawo loyamba. Chikalata chomwe wasainira wapampando wa bungweli, Justice Annabel Mtalimanja, chati MEC...
M’modzi mwa adindo ku unduna woona za madzi ndi zaukhondo, a Alexander Mwangonde, ati dziko la Malawi silikuchita bwino pa nkhani zaukhondo, zimene zikupereka chiopysezo...
Oyimba nyimbo zauzimu Steve Wazisomo Muliya wati nyimbo zotchyakuka bwino zitha kuthandiza kuchepetsa imfa za anthu amene amadzipha chifukwa cha nkhawa. Muliya, amene anapambana chaka...
Nduna yoona zachitetezo cha m’dziko, a Ken Zikhale Ng’oma, ati posachedwapa boma mogwirizana ndi dziko la China ligula zipangizo zomwe adziphunzitsira anthu amene ali ku...
Mtsogoleri wadziko lino, Dr Lazarus Chakwera, ali kwa mfumu yayikulu Kaphuka ku Dedza pamsonkhano wakalawe m’bomali. Polankhula kwa anthu ochuluka omwe anasonkhana pa sitolo za...
Three people have died after a minibus they were travelling in overturned on Monday along the Blantyre-Nsanje M1 Road. Chikwawa Police publicist, Dickson Matemba, says...
Timu ya Medina Stars yatenga chikho cha Ken Zikhale Ng’oma chimene ndi cha ndalama zokwana K6 million itagonjetsa timu ya Hauten 5-1 Lamulungu masana ku...
Mafumu ku Machinjiri m’boma la Blantyre awuza anthu awo kuti akalembetse mayina mu kaundula wachisankho amene akuchititsa a Malawi Electoral Commission (MEC). M’madera aku Machinjiri,...
Mtsogoleri wa timu ya Mighty Mukuru Wanderers, Thom Mpinganjira wapepesa otsatira timu yi chifukwa chogonja ndi timu ya FCB Nyasa Big Bullets dzulo loweluka ndizigoli...