Mtsogoleri wa dziko lino, Dr Lazarus Chakwera komanso mayi wa dziko lino Madam Monica Chakwera, alembetsa mu kaundula wa voti pa sukulu ya Malembo m’boma...
Wapampando wa bungwe la Malawi Electoral Commission (MEC), a Justice Annabel Mtalimanja, wapempha aMalawi kuti achotse chikayiko chimene angakhale nacho pa makina amakono akalembera wamavoti....
Mtsogoleri wa dziko lino, Dr Lazarus Chakwera, acheza ndi anthu m’madera angapo m’boma la Lilongwe, lero Lachitatu. Dr Chakwera ayambira kucheza ndi anthu a kwa...
Mlembi wamkulu wa chipani cha Malawi Congress (MCP), a Richard Chimwendo Banda, wati bata ndi mtendere ndi zofunika kwambiri pamene dziko lino likukonzekera chisankho cha...
Songwe Border United yaonjezera mwayi okhala akatswiri a mpikisano wa NRFA Simso-Mzuzu 12 itagongetsa timu ya Jenda United 2-0 dzulo pa bwalo lamasewero la Kangindwa...
Apolisi m’boma la Balaka anjata a Paul Lipenga, 46, powaganizira kuti anaononga komanso kuba nthambo za magetsi za ESCOM. Ofalitsa nkhani pa polisi ya m’boma...