Mtsogoleri wa Kabaza Association of Malawi (KAMA), a Joseph Petulo, wapempha mamembala awo amene ndi akabaza oposa 3.8 million, kuti apatule nthawi yawo ndi kupeza...
Mtsogoleri wa dziko lino Dr Lazarus Chakwera ndi Madam Monica Chakwera ali ku Abu Dhabi m’dziko la United Arab Emirates (UAE) kumene achite zokambirana ndi...
Mmodzi mwa omwe akufuna kupikisana nawo pa udindo wa phungu mdera la Mangochi Municipal pachisankho cha chaka cha mawa, Anussah Daddy Hassein, wadandaula ndi mchitidwe...
Pali kusamvana kunyumba ya malamulo pomwe aphungu akumbali yaboma ndi otsutsa akulephera kugwirizana kuti akambirane za kusintha kwa lamulo lakagulidwe ka mafuta agalimoto m’dziko muno....
Popitiriza kucheza ndi aMalawi m’madera osiyanasiyana, Prezidenti wa dziko lino Dr Lazarus Chakwera masana ano acheza ndi anthu m’madera angapo munzinda wa Lilongwe. Dr Chakwera...
Apolisi ku Chikwawa akufunafuna ophunzira omwe aphwanya ofesi ya mphunzitsi wamkulu pasukulu ya pulaimale ya Mitondo m’bomalo ati poganiza kuti mphunzitsi wamkuluyo akuchita zinthu za...