Category : Nkhani
‘Anthu opitilira 3,000 amwalira kaamba ka vuto la mpima’
Unduna wa zaumoyo wati kuyambira mu chaka cha 2019, anthu opitilira 3,400 amwalira m’dziko muno chifukwa chavuto la mpima. Vuto la mpima limadza pomwe tizilombo...
‘Achinyamata limbikirani’
Boma lati achinyamata akuyenera kuphunzira mozama ntchito zaluso ndi cholinga chakuti masomphenya adziko lino a 2063 akhale aphindu. Nduna yazachinyamata, a Uchizi Mkandawire, yalankhula izi...
DoDMA igawa matani 4,000 achimanga kwa amene njala yawakhudza
Nthambi ya DoDMA yatsimikiza kuti ifikira anthu onse amene akhudzidwa ndi njala m’dziko muno. M’modzi mwa akuluakulu ku nthambiyi, a Fyawupi Mwafongo, anena izi ku...
Wapha mwana wa zaka zitatu chifukwa chodutsa mmunda mwake
Apolisi ku Chiradzulu amanga John Tebulo wazaka 43 pomuganizira kuti wapha mwana wazaka zitatu kaamba kodutsa mmunda mwake. Ofalitsankhani wapolisi ku Chiradzulu, Cosmas Kagulo, wati...
A Bango ayamika Dr Chakwera chifukwa choganizira anthu a m’boma la Kasungu
Phungu wadera lakumpoto m’boma la Kasungu, a Mike Bango, ayamika mtsogoleri wa dziko lino Dr Lazarus Chakwera yemwenso ndi mtsogoleri wa chipani cha Malawi Congress,...
Mbeu zamakolo zikuchepa — Kafufukufuku
Kafukufuku yemwe ophunzira a sukulu ya ukachenjede ya Lilongwe University of Agriculture and Natural Resources (LUANAR) achita mogwirizana ndi mabungwe amene amaona ntchito zosamalira chilengedwe...

