Bungwe la Malawi Revenue Authority (MRA) lati likwanitsa kutolera ndalama zokwana K2.18 trillion mu chaka cha boma cha 2023/2024 chimene chikutha kumapeto a mwezi uno....
Mmodzi mwa akuluakulu ku bungwe lowona zakasamalidwe kazinyalala la Waste Advisors, a John Chome, ati dziko la Malawi lili ndikuthekera kopeza phindu lochuluka kuchokera ku...
Apolisi m’boma la Mchinji anjata m’busa wa Bua Abraham Africa yemwe dzina lake ndi James Solomon pomuganizira kuti anaba waya wa magetsi wa kampani ya...
Bwalo la Magistrate ku Lilongwe likupitilira kumva mboni za boma pa mlandu wa a Norman Chisale, yemwe anali wachitetezo wa mtsogoleri opuma. Nduna yoona za...
Apolisi ku Namwera m’boma la Mangochi atsekera m’chitokosi a Nelson Lipenga azaka 49 zakubadwa powaganizira kuti akhala akugwilira ophunzira wa zaka 15 wa Standard 8...
Mtsogoleri wa zokambirana za m’nyumba ya malamulo a Richard Chimwendo Banda ati nthawi yakwana ku chipani cha Democratic Progressive (DPP) kuti apatseko mpata achinyamata popereka...
President Dr Lazarus Chakwera wathokoza Sinodi ya Livingstonia ya mpingo wa CCAP chifukwa chothandiza boma pa ntchito zosiyanasiyana za chitukuko. Poyankhula pa mwambo wa mapemphero...