Apolisi aponya utsi okhetsa misonzi pobalalitsa anthu omwe anayambitsa zipolowe ku tchalitchi ya mpingo wa CCAP ya M’bawa ku Mbayani mu mzinda wa Blantyre. Izi...
Nduna ya maboma ang’ono, umodzi ndi chikhalidwe, yomwenso mkulu woona za achinyamata mchipani cha Malawi Congress (MCP), a Richard Chimwendo Banda, yati boma la Dr...
A Mapulani Nkosi aku Mzimba akusimba lokoma kaamba kochita ulimi wa mpunga m’bomali, lomwe ambiri amalidziwa ndi ulimi wa fodya komanso mtedza. A Nkosi, amene...
A Ken Msonda, omwe alandiridwa ku chipani cha Malawi Congress MCP dzulo, ati ndi odabwitsidwa ndi chilimbikitso chimene apatsidwa ndi mafumu akuluakulu a m’boma la...
Unduna wa zamalimidwe wati wakonza ndi kuunikanso ndondomeko ya chuma yomwe anaikonza kuti agulire chimanga chaka chino. A Geoffrey Mamba, amene ndi mlembi ku undunawu,...
M’modzi mwa amene anali mamembala akuluakulu achipani cha DPP, a Ken Msonda, alowa chipani cha Malawi Congress (MCP). A Msonda alandiridwa m’chipani cha MCP ku...
Mtsogoleri wa dziko lino, Dr Lazarus Chakwera, walimbikitsa anthu amene ngozi yakusefukira kwa madzi yawakhudza kuti asaganize zodzipha komanso asataye mtima. A Chakwera ati iwo...