Category : Nkhani
Zinthu zambiri zasintha — Chithyola Banda
Nduna yoona zachuma, a Simplex Chithyola Banda, ati zinthu zambiri zasintha ndipo chuma chayamba kubwelera m’chimake. Iwo amayankhapo pa lipoti la bungwe la Afrobarometer...
Zipani zikusowekera demokalase ndi umodzi, CCAP ya Livingstonia Sinodi yatero
Sinodi ya Livingstonia mu mpingo wa CCAP, pansi pa nthambi yake ya chilungamo ndi mtendere, yati mu zipani zambiri m’dziko muno mulibemo demokalase ndi umodzi....
Zamanyazi: Mphunzitsi ogwililira akagwira ukaiyidi kwa zaka 20
Bwalo la milandu m’boma la Mangochi lalamula a Nelson Lipenga kuti akagwire ukaidi wa kalavula gaga kwa zaka makumi awiri (20) kaamba kopezeka olakwa pa...
Malawi yapeza $2 million kuchokera ku Israel
Photo Credit : Gianluigi Guercia Pofika mwezi uno, dziko la Malawi lapeza ndalama zokwana $2 million (pafupifupi K3.4 billion) kuchoka ku ndondomeko yotumiza achinyamata kukagwira...
Prezidenti Chakwera ayendera chitukuko m’boma la Mzimba
Mtsogoleri wa dziko lino, Dr Lazarus Chakwera, lero apita m’boma la Mzimba kumene ayendere ntchito yomanga bwalo lazamasewero la M’mbelwa kudzanso ofesi za khonsolo ya...
“Ntchito zomangamanga zidzikhala zapamwamba”
Prezidenti wadziko lino, Dr Lazarus Chakwera, wati ndikofunika kuti makontalakitala adzigwira ntchito zapamwamba ndi zolimba. Pa chifukwachi, Dr Chakwera walamula mlembi mu ofesi ya Prezidenti...
Namondwe Filipo alibe chiopsezo ku Malawi, atero azanyengo
Nthambi yoona za nyengo m’dziko muno yatsimikiza kuti namondwe Filipo safika m’dziko muno. Nthambiyi yati namondweyu akuyenda mobwelera ku nyanja ya mchere ya India, komwe...

