Malawi Broadcasting Corporation
Nkhani

Prezidenti Chakwera ayendera chitukuko m’boma la Mzimba

Mtsogoleri wa dziko lino, Dr Lazarus Chakwera, lero apita m’boma la Mzimba kumene ayendere ntchito yomanga bwalo lazamasewero la M’mbelwa kudzanso ofesi za khonsolo ya M’mbelwa m’bomalo.

Dr Chakwera akafikanso kulikulu la Inkosi yamakhosi M’mbelwa.

Mtsogoleri wa dziko linoyu akucheza m’chigawo chakumpoto ndikuyendera ntchito za chitukuko zosiyanasiyana.

Related posts

Agwidwa ndi mankhwala oopsya ozunguza bongo

Tisunge bata, mtendere — Inkosi ya Makosi Goman V

Mayeso Chikhadzula

‘Dekhani pa bizinesi’

Rabson Kondowe
error: All Content is protected. Copyright © 2022. Malawi Broadcasting Corporation. All Right Reserved.