Bungwe la Football Association of Malawi lero lapepesa ku Goshen Trust, yomwe imathandiza mpira wamiyendo wa atsikana, kaamba kochedwa kudzaonetsa chikho cha COSAFA chomwe timu...
Prezidenti wa dziko la Tanzania Samia Suluhu Hassan apempha maiko a mu Africa kuti apitilize kugwirizana, poti kutero kuthandiza kutukula Africa. Mtsogoleriyu wanena izi pa...
Mkulu wa kampani ya Old Mutual m’dziko muno, a Edith Jiya, ati dziko lino likuyenereka kuti likonze mavuto a magetsi komanso misonkho pofuna kuti dzikoli...
Mkulu wa MBC a George Kasakula ati malemu Geoffrey Kapusa anali munthu yemwe anali katakwe pantchito youlutsa mawu pa kanema komanso kuongolera tsogolo lankhani zoulutsa...
Nduna yoona zamphamvu zamagetsi, a Ibrahim Matola, yomwe imachita nawo msonkhano waukulu wamaiko apa dziko lonse wokambirana zamphamvu zamagetsi wa World Energy Congress ku Rotterdam...
Apolisi m’chigawo chakummwera amanga Richard Herema wazaka 42, yemwe kwawo ndi ku Mozambique, pomuganizira kuti iyeyo pamodzi ndi amzake,l anathyola nyumba ziwiri ndikuba ndalama zoposa...
Apolisi mu mzinda wa Zomba amanga a Andrew Banda a zaka 25 zakubadwa powaganizira kuti anagwirira mwana wazaka 12. Ofalitsankhani wa Polisi ya Zomba, a...