“Ndikofunika kuti a Malawi adzikondana komanso kuthandizana pa mavuto ndi mtendere,” awa ndi mawu amene anena ndi eni ake a kampani ya Sosten Motors, a...
A Mtiuze Chapondera a zaka 30 am’dera la Group Village Headman Chimwendo kwa mfumu yaikulu Masumbankhunda ku Lilongwe akuti akwanitsa kuchotsa banja lawo mu umphawi...
Mwini wake wa kampani ya New Dawn Boxing promotion, Michael Chimaliza, wapempha mabungwe komanso kampani zosiyanasiyana m’dziko muno kuyika chidwi potukula masewero omwe amaoneka ngati...
Maanja oposera 20,000 kuchokera mmagulu osunga ndi kuchulukitsa ndalama omwe ali pansi pa bungwe la COMSIP akuyembekezeka kupeza zokolora zochuluka kaamba ka zipangizo za ulimi...
Mmodzi mwa oimba nyimbo za achinyamata, Zonke Too Fresh, watulutsa kanema wa nyimbo yake yatsopano yotchedwa Vote. Mu nyimboyi, Zonke Too Fresh, yemwe dzina lake...
Nduna yaza mtengatenga, a Jacob Hara, yati sitima yoyenda pakati pa mizinda ya Blantyre ndi Lilongwe iyambiranso posachedwapa. A Hara anati gawo lachiwiri ikhala kukonzanso...
Nduna yoona za maboma aang’ono komanso umodzi ndi chikhalidwe, a Richard Chimwendo Banda, yati siyokhutitsidwa ndi m’mene gawo lina la msewu wa Chiwembe mu mzinda...
Bungwe la Malawi Red Cross Society lapeleka ndalama zokwana K250,000 kwa mabanja okwana 724 ku Karonga ngati thandizo kutsatira ngozi ya kusefukira kwa madzi yomwe...
Bungwe la Malawi Union of Savings and Credit Cooperatives (MUSCCO) lati chuma chama SACCO tsopano chakwana K82 billion chaka chino chokha kuchokera kwa mamembala okwana...