Category : Nkhani
Ntchito za manja zikuthandiza kusintha miyoyo ya achinyamata
Eunice Katunga wa ku Lunzu m’dela la Group Village Headman Kumponda mfumu yaikulu Kapeni m’boma la Blantyre wati moyo wa banja lake wasintha potsatira ntchito...
Musapereke za unzika kwa aliyense — Kunkuyu
Boma ladzudzula m’chitidwe omwe anthu ena akumachita otenga ziphaso za unzika za anthu ena powanamiza kuti awamangira nyumba, mwa zina. Nduna yofalitsa nkhani, a Moses...
Thandizani mpira wa m’maboma — CRFA
Bungwe la Central Region Football Association (CRFA) lapempha anthu okonda mpira wa miyendo m’dziko muno kuti abwere poyera ndikuthandiza mpira wa m’maboma. Mlembi wamkulu wa...
Athana ndi umphawi pokonza sopo
Amayi anayi ochokera kwa Gavi m’dera la mfumu Kapeni m’boma la Blantyre akupha makwacha atatsekula bizinesi yawo yopanga sopo pofuna kuthana ndi umphawi. Amayiwa adachita...
Mlandu wa Bushiri wayima kaye!
Bwalo lamilandu la Chief Resident Magistrate ku Lilongwe layamba laima kaye kumva mulandu omwe boma la South likufuna kuti Banja la a Bushiri lipite mdzikolo...
MBC ikuchita bwino — Chiyamwaka
Unduna wazofalitsa nkhani wati ndiokhutira ndi m’mene MB ikugwirira ntchito zake pokwaniritsa zokhumba za aMalawi onse m’dziko muno. Mlembi wamkulu mu undunawu, a Baldwin Chiyamwaka,...
Khonsolo ikufuna ndalama za chitukuko zidzibwera motsata ndondomeko
Akuluakulu a khonsolo ya m’boma la Nkhotakota ati kulandira kwa ndalama zachitukuko mopelewera komanso mopanda ndondomeko kukusokoneza magawo ambiri akagwiridwe kawo kantchito m’bomali. DC wa...
Feteleza wa Mbeya wasintha banja la a Thabwa modabwitsa
A Tsazo Thabwa a m’mudzi mwa Fayifi kwa mfumu yaikulu Dzoole B m’boma la Dowa akuti moyo wa pa banja lawo wasintha modabwitsa potsatira zokolora...
Amumanga ataba mu kachisi
Apolisi ku Lilongwe amanga mwamuna wazaka 44, Patrick Zgambo, pomuganizira kuti waba zipangizo zoyimbira za ndalama pafupifupi K3.5 million za tchalitchi chotchedwa Time of God....

