Alimi ang’ombe za mkaka mmadera a Satemwa ku Thyolo ndi Mpemba ku Blantyre ati milatho yomwe bungwe la TRADE Programme lamanga mmadera awo ithandiza kuti...
Mphunzitsi wamkulu wa sukulu ya Kasitu CDSS, imene ili kudera la kumpoto m’boma la Nkhotakota, a Mixom Gama, ati ophunzira wawo Owen Nkhoma analephera kulipira...
Kampani ya lamya za mmanja ya TNM yalengeza kuti ipereka mabandulo a chipukutamisonzi kwa makasitomala ake oposa 1million kamba kopilira ku vuto la internet limene...
Wachiwiri kwa Mtsogoleri wa dziko la Iran a Mohammad Mokhber nde mtsogoleri watsopano wa dzikoli kutsatira imfa ya mtsogoleri wawo a Ebrahim Raisi pa ngozi...
Alimi a ng’ombe za mkaka a ku Mangunda m’boma la Thyolo ati akuyembekeza kuti phindu la ulimi wawo lichuluka kaamba kakuti pa malowa ayikako magetsi...
Apolisi ku Chiradzulu amanga mphunzitsi wazaka 36, Daniel William, wa pa sukulu ya pulayimale ya Chawe pomuganizira kuti anaba ndalama zokwana K67,150 zolipilira mayeso a...
Lero masana ikamakwana 2:30, matimu a Silver Strikers ndi Mighty Mukuru Wanderers athambitsana pabwalo la Silver mu mzinda wa Lilongwe. Silver, yomwenso imatchedwa kuti Mabanker,...
Lero ndi tsiku lokwangula ligi ya ku Engalnd pamene m’modzi mwa matimu a Arsenal ndi Manchester City avekedwe ufumu wa ligiyi. Manchester City ndi imene...
Anyamata awiri, Dziwani Mwachumu ndi Kenneth Banda, adzitama kuti apalasa njinga kuchokera mumzinda wa Lilongwe kukathera mumzinda wa Blantyre kwa masiku awiri. Iwo ati achita...