Akatswiri azachuma komanso ufulu wachibadwidwe ayamikira boma chifukwa ka ndondomeko zoyenera zokonzeranso chuma cha dziko lino zomwe akuti zapangitsa a World Bank kupereka thandizo la...
World Bank yapereka 80 million dollars (imene ndi pafupifupi K140 billion) ku boma la Malawi zothandizira pa ntchito zake zokweza chuma ndi miyoyo ya anthu...
Banja la bambo ndi mayi Loyd lathokoza chipatala cha boma cha Bwaila chimene chinathandiza mayi Loyd omwe anadwalako matenda a Kadzamkodzo. Adindo apa chipatalachi adawapatsakonso...
Dziko la Malawi, pamodzi ndi maiko ena onse padziko lapansi, lero akukumbukira tsiku la matenda a kadzamkodzo, amene pachingelezi amatchedwa kuti Fistula. Tsikuli layamba ndi...
Mtsogoleri wa dziko lino, Dr Lazarus Chakwera akuyembekezeka kufika ku Chichiri Trade Fair Grounds komwe atsegulire chionetsero cha za malonda. Bungwe la Malawi Confederation of...
Bungwe lothana ndi ziphuphu ndi katangale m’dziko muno la ACB lati kumpira kumachitika zachinyengo zosiyanasiyana zimene zikupangitsa kuti zamasewero zisamapite patsogolo. Mkulu wa bungweli, Martha...
Bungwe la Malawi Bureau of Standards (MBS) lati ndipofunika kuti zipatala za m’dziko muno zidzikhala ndi zipangizo zoyezera zosonyeza milingo kapena kulemera kwa zinthu komanso...
Khonsolo ya mnzinda wa Lilongwe yati sizoona kuti ogwira ntchito ku khonsoloyi amagawana katundu yemwe alanda kwa anthu ogulitsa malonda m’malo osayenera. Mfumu yamnzinda wa...
Mamembala a magulu 16 a Community Savings and Investment Promotion (COMSIP) akonzetsa madesiki 65 pa sukulu ya pulaimale ya Chivutwe, imene ili m’mudzi wa Mdwala,...
Bungwe la maiko akumwera kwa mu Africa la Southern Africa Development Community (SADC) lati mphepo ya El Niño yadzetsa mavuto ambiri omwe akhudza anthu opitilira ...