Mtsogoleri wa dziko lino Dr Lazarus Chakwera wapempha aMalawi kuti agwirizane ndi kuyenda limodzi ndi anthu omwe ali ndi chidwi chofuna kumanga dziko lino kuti...
Apolisi ku Soche mu mzinda wa Blantyre amanga Mervin Sulemani wa zaka 27 pomuganizira kuti anapha Rizwani Issa pomukhapa pa 21 mwezi uno ku Chinyonga....
Mfumu yaikulu Mwamulowe ya m’boma la Rumphi yapempha anthu omwe akukhala m’madera ena ochokera ku dera lake kuti adzikumbukira mavuto omwe ali kuderali ndikumachitapo kanthu....
Apolisi ku Nkhunga m’boma la Nkhotakota amanga amuna awiri powaganizira kuti amatsatsa malonda a mwana wazaka zitatu. Mneneri wapolisi ya Nkhunga, Andrew Kamanga, wati amunawo...
Nduna ya za m’dziko, a Ken Zikhale Ng’oma, yalonjeza anthu ku Nsanje kuti boma lipitilira kukhazikitsa ntchito za chitukuko m’bomali ndi cholinga chotukula bizinesi zawo....
Phungu wa dera lakummawa kwa boma la Rumphi, a Kamlepo Kalua, ayamikira mtsogoleri wa dziko lino, Dr Lazarus Chakwera, chifukwa cholora bungwe la MACRA kuti...