Woimba wachichepere Sife Mw, yemwe dzina lake lenileni ndi Silvia Sifenjanie Sande ndipo ali ndi zaka 21, wati nyimbo yake yatsopano ndi bvumbulutso loti litonthoze...
Apolisi ku Zomba amanga a Jaru Kambanga, 36 ndi a Patrick Bwanali, 31 powaganizira kuti anagwililira komanso kuba katundu wina pa malo ogona atsikana a...
Akuluakulu apa chipatala chachikulu cha Mzuzu ati chipatalachi chikulandira abambo pafupifupi 60 mwezi uli ofuna chithandizo cha nthenda ya khansa ya chida cha abambo, penile...
Wupu wa MACRA wati wawika ndalama zakukwana 6 billion kwacha mu chigawa chakwamba cha mlimo wakuzenga vipinda vyakusambiliramo unkhwantha wa sono ivyo vikuzengeka msukulu 75...
Mphunzitsi wamkulu wa timu ya Mighty Mukuru Wanderers, Nsazurwimo Ramadhan, wati watula pansi udindowu kutsatira kugonja kwa timuyi mumasewero awiri motsatizana mu TNM Super League....
Nduna yoona za maboma ang’ono, umodzi ndi chikhalidwe cha anthu a Richard Chimwendo Banda ati thandizo la ndalama zokwana $80 million ndi chitsimikizo choti World...
Phungu wadera la kumadzulo m’boma la Mwanza, Joyce Chitsulo, wayamikira boma chifukwa chogawa chitukuko mosayang’ana chipani. A Chitsulo, amene ndi phungu wa chipani cha Democratic...
Mtsogoleri wa dziko lino Dr Lazarus Chakwera wapempha aMalawi kuti agwirizane ndi kuyenda limodzi ndi anthu omwe ali ndi chidwi chofuna kumanga dziko lino kuti...