Bungwe la Oxfam lati lalandira K650 million yoti igwire ntchito yothandizira ndondomeko yolimbikitsa amayi kutenga nawo gawo pandale. Mkulu wa bungweli a Lingalireni Mihowa, wanena...
Mtsogoleri wa dziko lino Dr Lazarus Chakwera wapereka ndalama zokwana K5 million kuti zithandizire pamwambo wa maliro a Raphael Kasambara omwe atisiya masiku apitawa. A...
Synod ya Blantyre ya Mpingo wa CCAP tsopano yaonjezera chiwerengero cha abambo omwe ndi mamembala a Utumiki wa Abambo, potsatira kupatulidwa kwa gulu la abambo...
Mwambo wa mapemphero otsanzikana ndi katswiri pa zamalamulo Ralph Kasambara wayamba ku CI mu mzinda wa Blantyre. Akuluakulu osiyanasiyana kuphatikizapo a boma, a zipani za...
Majaji m’dziko muno ati ali ndi chisoni kaamba ka imfa ya a Raphael Kasambara omwe anali katswiri wa za malamulo komanso yemwe anathandiza kwambiri polimbikitsa...
Davis Lungu wakhala wachinyamata wachinayi kupeza mpamba oyambila malonda wa ndalama zokwana K1 million yomwe ili muntchito yothandiza achinyamata 18 powapatsa K1 million aliyense kuti...
Khonsolo ya mzinda wa Mzuzu yati ikufuna kutolera ndalama zokwana K2.4 billion kuti igwire bwino ntchito zake zachitukuko,pansi pa ndondomeko yake ya chuma ya 2024/2025....
Mpikisano wa masewero a mpira wamanja komanso miyendo wa ophunzira msukulu za ku Machinjiri wa South Lunzu Primary Schools Trophy, wayamba ndi ntibu wa zigoli...