Timu ya mpira wamiyendo yadziko lino yanyamuka kupita m’dziko la Equatorial Guinea komwe akasewere ndi timu yadzikolo mumpikisano wodzigulira malo wapadziko lonse. Timuyi ikagona ku...
Sukulu ya sekondale ya private ya Maranatha Academy ndi yomwe yatumiza chiwerengero chachikulu cha ana omwe awasankha kuti akayambe maphunziro aza ukachenjede kusukulu zosiyanasiyana m’dziko...
Bungwe la alimi a fodya la TAMA Farmers Trust layamikira mtsogoleri wa dziko lino Dr Lazarus Chakwera poonetsetsa kuti alimi a fodya akugulidwa fodya pa...
Bwalo la High Court Ku Lilongwe lagamula kuti a Anne Mumba ndi wolakwa pamlandu woti ndiwo adapha amuna awo, malemu Professor Peter Mumba. Justice Mzondi...
Mkulu wa nthambi yoona zamaulendo apa ndege m’dziko muno (Department of Civil Aviation), a Vetrus Francis Dziwe, wati ntchito za maulendo apa ndege zikuyenda bwino...
Phindu la kampani ya Illovo Sugar Malawi latsika kufika pa K32.5 billion mu miyezi ya pakati pa September chaka chatha mpaka February chaka chino, kuchoka...
Bungwe la National Registration Bureau lati lalemba anthu 1,556,613 pa ndondomeko ya kalembera ya chiphaso cha unzika. Mlembi wamkulu wa bungwe la National Registration Bureau,...