Malawi Broadcasting Corporation
Nkhani

Dr Chakwera apereka K5 million zothandizira pamaliro a Kasambara

Mtsogoleri wa dziko lino Dr Lazarus Chakwera wapereka ndalama zokwana K5 million kuti zithandizire pamwambo wa maliro a Raphael Kasambara omwe atisiya masiku apitawa.

A Harry Mkandawire, amene akuyimira Dr Chakwera, ati malemu a Raphael Kasambara anali munthu okonda kumenyera ufulu wa anthu osauka.

Iwo ati boma lisowa ntchito zambiri zomwe malemuwa anathandizirapo maaka pa chitukuko.

A Mkandawrire ayankhula izi pamene mwambo wa maliro uli mkati m’boma la Nkhata Bay.

Related posts

Dr Usi ati adzipereka pofuna kukweza miyoyo ya a Malawi

Romeo Umali

Msonkhano waukulu tichita mu September — JB

Romeo Umali

Boma lagawa chimanga ku Zomba

Rabson Kondowe
error: All Content is protected. Copyright © 2022. Malawi Broadcasting Corporation. All Right Reserved.