Limodzi mwa mabungwe omwe si a boma lotchedwa M’badwa Zokhudzidwa lapempha zipani zonse zandale kuti zipereke ulemu oyenera kwa wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino,...
Galimoto yomwe yanyamula malemu Dr Saulos Chilima kubwalo lazamasewero la Bingu National lanyamuka pa mdipiti kupita kumudzi kwawo kwa Mbirimtengerenji mdera la mfumu yaikulu Champiti...
Nduna yoona zachitetezo m’dziko la Zambia, a Ambrose Lwiji Lufuma, yati dziko lawo lili ndi chisoni chachikulu chifukwa cha imfa ya wachiwiri kwa mtsogoleli wa...
Bungwe loona za chisankho mdziko muno la MEC lati anthu amene akuyembekeza kuponya voti pa chisankho cha makhansala ku Mwasa Ward m’boma la Mangochi ndi...
Mtsogoleri wa dziko lino, Dr Lazarus Chakwera pamodzi ndi Madame Monica Chakwera, watsogolera mtundu wa aMalawi powona nkhope ya wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino,...
Bambomfumu apa Parish ya St Patrick’s mu mzinda wa Lilongwe, a Henry Zulu, alangiza Akhristu m’dziko muno kuti atengere chitsanzo chabwino cha moyo wa wachiwiri...
Ku St Patrick’s Parish, zonse zokonzekera kulandira thupi la Dr Saulos Chilima zatha. Padakalipano, anthu ochuluka afika kudzakhala nawo pa misa ya maliro a wachiwiri...
Nduna yazofalitsa nkhani yalengeza kusintha kwina kwa ndondomeko ya momwe mwambo wa maliro a Dr Saulos Chilima uyendere. Mwa zina, a Kunkuyu ati mtsogoleri wa...