Pamene mwambo wokhuza maliro a wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino, malemu Dr Saulos Chilima, ukupitilira ku Area 12, mtsogoleri wa bungwe la Mayi Maria...
Thupi la malemu Patricia Shanil Dzimbiri alitengera ku mudzi kwa Mfulanjobvu, kwa Kangamkundi m’dera la mfumu yayikulu Chamthunya m’boma la Balaka komwe akaliyike m’manda. Kuyambira...
Mtsogoleri wa dziko lino, Dr.Lazrus Chakwera, akhala nawo pamwambo wa nsembe ya Misa ya mayi Shanil Dzimbiri kunyumba ya chisoni ya Sunrise ku Kanengo munzinda...
Mwambo wa mapemphero uli mkati ku nyumba yachisoni ya Sunset ku Kanengo, omwe ndi mwambo wofuna kuperekeza matupi a omwe adamwalira pa ngozi ya ndege...
Anthu ochuluka asonkhana ku nyumba ya chisoni ya Sunset Funeral Services ku Kanengo munzinda wa Lilongwe komwe pali chikonzero chonyamula ena mwa matupi a anthu...
Mkulu wa kampani ya Airtel Malawi, Charles Kamoto, wati malemu Dr Saulos Chilima anali munthu wodzipereka ndi wokonda ntchito. Poyankhula ndi MBC, a Kamoto ati...
Chipani cha UTM chati ndipofunika kuti pakhale umodzi pakati pa anthu onse m’dziko muno pofuna kuti mwambo wokhuza wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino malemu...
Bambo mfumu Henry Zulu aku St. Patrick Parish ku Area 18 ati malemu Dr Saulos Chilima anali olimbikira pogwira ntchito zampingo komanso kutumikira dziko. Iwowa...
M’mawa uno, nduna yofalitsa nkhani, a Moses Kunkuyu, anali nawo pa mwambo operekeza maliro a Abdul Lapukeni kuchoka munzinda wa Lilongwe. A Lapukeni, omwe ndi...