Thupi la yemwe anali ochita zisudzo komanso muulutsi, malemu Hope Chisanu, lafika m’dziko muno kudzera pa bwalo la ndege la Kamuzu International Airport munzinda wa...
Katswiri omwetsa zigoli wa timu yampira wa miyendo ya amayi, Tabitha Chawinga, akhale akusewelera timu ya Lyon ya mdziko la France pomwe wachita mgwirizano wa...
M’nyamata wazaka 17 zakubadwa, Tinasha Mtawali, wafa atadziombera ndi mfuti ya mtundu wa pistol ku Chitipi munzinda wa Lilongwe chifukwa anasemphana chichewa ndi bwenzi lake,...
Charles Sinetre ndimmodzi wa akatswiri amene adayimba limodzi ndi malemu Lucius Banda. Kodi adzamukumbukira motani? Olembankhani wathu Simeon Boyce anacheza ndi Sinetre motere: Q-Kodi ndi...
Wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino Dr Michael Usi wamema a Malawi kuti adzipempherera mtsogoleri wathu Dr Lazarus Chakwera komanso a Mary Chilima pa nthawi...
Phwando lolimbikitsa luso ndi chikhalidwe lodziwika kuti Khulubvi Arts and Cultural Festival, lomwe layamba dzulo lachisanu pa 28 June ndipo litha mawa pa 30 June...
Gulu la amayi ochita mapemphero a pachaka la Women’s World Day of Prayer la m’chigawo chapakati lapereka thandizo lokwana K5.5 million kwa ana aulumali pa...