Category : Nkhani
Malinga Mafia wapepesa atachedwa ku Illusionz
Katswiri oyimba Dancehall, Malinga Mafia, wapepesa kwa okonda nyimbo zake kaamba kokanika kuyimba ku phwando lamayimbidwe la Illusionz lomwe likuchitikira pagombe m’boma la Mangochi. Katswiriyu...
‘Kanema wa Belinda alimbikitsa atsikana’
Amene anajambula kanema wa Belinda, gulu la Remnant Lions, ati ali ndi chikhulupiliro kuti kanemayu alimbikitsa atsikana kuti asamafooke pa maphunziro ngakhale atakumana ndi mavuto,...
‘Mgwirizano ndi ofunika pa ntchito yobwezeretsa chilengedwe’
Bwanamkubwa wa boma la Neno, Rosemary Nawasha, wati adindo m’bomalo akugwilira ntchito limodzi pofuna kuthana ndi mchitidwe owononga zachilengedwe komanso kubwezeretsa chilengedwe . A Nawasha...
‘Dekhani pa bizinesi’
Achinyamata omwe alandira mpamba wa ndalama zokwana K1 million aliyense kuchokera kwa Triephornia Mpinganjira pansi pa ndondomeko ya ‘kuthandiza omwe alibe kuthekera kupita patsogolo’ awalangiza...
Bwezani ngongole kuti ena apindule — NEEF
Bungwe la National Economic Empowerment Fund (NEEF) lati zomwe anthu ena akufalitsa kuti boma lakhululukira onse omwe anatenga ngongole ku NEEF kuti asabweze ndi zabodza....
Illovo ithandiza okhudzidwa ndi kusefukira kwa madzi ku Nkhotakota
Anthu amene anakhudzidwa ndi ngozi ya kusefukira kwa madzi chaka chino ku Dwangwa m’boma la Nkhotakota alandira katundu osiyanasiyana wa ndalama zokwana K100 million kuchokera...
Lipoti lokhudza ngozi ya ndege ku Chikangawa yatuluka
Bungwe la German Federal Bureau of Aircraft Accident Investigation (BFU) latulutsa lipoti la ngozi ya ndege imene inachitikira mu nkhalango ya Chikangawa m’boma la Mzimba,...

