Mwambo wa misa ya maliro a malemu bambo Claude Boucher Chagomerana Chisale watha pabwalo la Kungoni m’boma la Dedza. Poyankhula, nduna yoona za malo, a...
Komishonala wa DoDMA, a Charles Kalemba, walangiza makomiti othandiza anthu kuti adziwonetsetsa kuti okhawo okhudzidwa ndi ngozi zakugwa mwadzidzidzi ndi amene akulandira thandizo. A Kalemba...
Nthambi ya boma yoyang’anira mabungwe a masewero yati bwalo la makono la masewero la BAT lomwe boma likumanganso mu mzinda wa Blantyre muzidzalowa anthu okwana...
Mfumu yaikulu Nkhulambe ya m’boma la Phalombe yamwalira usiku wapitawu. Malinga ndi bwanamkubwa wa boma la Phalombe, a Douglas Moffat, Mfumu yaikulu Nkhulambe yamwalira itadwala...
Komiti yoona za chilengedwe ndi kusintha kwa nyengo yauza nyumba ya malamulo kuti dziko la Malawi likuyenela ku kweza pang’ono mtengo wogulira mafuta a galimoto...
Bungwe la Technical Entrepreneurial Vocational and Education Training Authority (TEVETA) likulingalira zolimbikitsa ndondomeko yofuna kuti maphunziro a ntchito za manja afikire anthu onse. Wapampando wa...
Apolisi kwa Namalaka m’boma la Mangochi amanga Mofolo Yohane,22, yemwe ndi msodzi pomuganizira kuti anakhapa m’mutu Bashir Haji, wa zaka 13, ndi cholinga chakuti amuphe...
Mkulu oona za chisankho ku chipani cha UTM, Happy Kondowe, wati zomwe achita mamembala ena achipanichi kulengeza tsiku la pa 17 November chaka chino ngati...
Masewero ndi njira yabwino yofalitsira mauthenga a uchembere wabwino komanso kudziwa za ma ufulu a achinyamata pa nkhani zogonana komanso banja, bungwe la Umunthu Foundation...