Zidutswa za ndege imene inasowa itangonyamuka kumene pa bwalo la ndege la Vachkazhets m’dziko la Russia azipeza. Malinga ndi unduna owona za ngozi zogwa mwadzidzidzi...
Wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino, Dr Micheal Usi, ayamikira ndi kuthokoza mpingo wa Anglican pogwira ntchito ndi boma m’magawo osiyanasiyana a chitukuko. Dr Usi...
Msonkhano waukulu wa mpingo wa CCAP mu Sinodi ya Livingstonia anayamba awuyimitsa kaye moderator watsopano wa sinodiyi, m’busa Jairos Kamisa, atadzudzula akuluakulu a mpingowo ‘chifukwa...
Bungwe la Malawi Network of People Living with HIV and AIDS (MANET+) lapereka njinga yamoto ku ofesi ya zaumoyo ya Mzimba North yomwe ithandizire pantchito...
Nduna ya zofalitsa nkhani yomwenso ndi mneneri wa boma, a Moses Kunkuyu akuchititsa msonkhano wa atolankhani ku Lilongwe pa lipoti la ngozi ya ndege yomwe...
Ofesi yoona zofalitsa nkhani mu ofesi ya mlembi wamkulu wa boma ndi nduna OPC yalangiza atolankhani kuti apitirize kugwira bwino ntchito ndi boma. Mneneri wa...
Akuluakulu a mpingo wa CCAP mu synod ya Livingstonia akukumana ku Embangweni ku tchalichi cha Laudon m’boma la Mzimba. Moderator wa Mpingowu M’busa Rueben Msowoya...
Mpingo wa Manja Seventh Day Adventist mu nzinda wa Blantyre lero ukumalizitsa msonkhano wake wa pachaka wa Misasa omwe unayamba pa 27 August 2024. Mutu...
Mwambo wa chionetsero cha ntchito zokopa alendo komanso chikhalidwe wayamba ndi ulendo wa ndawala kuchokera pa Memorial Tower mpakana mu msewu wa Presidential Drive munzinda...
Bwalo la milandu la First Grade m’boma la Mzimba lalamula a Emmanuel Khowaya,32, kuti akagwire ukayidi wa kalavula gaga kwa zaka khumi ndi ziwiri atawapeza...