Bungwe la ESCOM lati makina ake a magetsi anadzithimitsa lero nthawi itatsala mphindi 18 kuti ikwane 12 koloko masana. Malinga ndi chikalata chomwe a ESCOM...
Mkulu oyang’anira zomangamanga ku unduna wa zaumoyo, Dr Sanderson Kuyeli, wati gawo loyamba pantchito yomanga chipatala cha Mponela Community m’boma la Dowa latsala pang’ono kutha....
Apolisi ya Lingadzi ku Lilongwe agwira anthu asanu ndi atatu amene akuwaganizira kuti ndi amene akhala akubera anthu pa msewu wa ABC, umene ndi ochokera...
Osewera wakale watimu ya Silver Strikers Mike Robert, wamwalira kamba kavuto la impso kuchipatala cha Kamuzu Central munzinda wa Lilongwe. Mng’ono wake wa Mike, Jacob,yemwe...
Bungwe la Malawi Confederation of Chambers of Commerce and Industry (MCCCI) lati alimi osiyana apeza misika ya ndalama zokwana K900 million pachiwonetsero cha zaulimi chomwe...
Anthu okhala dera la Manja mu mnzinda wa Blantyre ati ndiokondwa ndi ganizo la boma lofuna kuyamba ntchito yomanga nsewu kuderali. Boma kudzera ku khonsolo...