Key stakeholders are reviewing the Last Mile Infrastructure Pre-Feasibility Report for the Southern Africa Trade and Connectivity Project (SATCP) in Dowa. The meeting, chaired by...
Timu ya masewero a Draughts ya dziko lino yalephera kupita kukasewera nawo mpikisano wa dziko lonse kaamba kochedwa kukonzekera. Mlembi wa bungwe loyendetsa masewero wa...
Gulu la akatswiri oyimba nyimbo zauzimu osachepera 50 amene adakumana koyamba mu 2020, tsopano akhazikitsa Hephzibah Worship Band. Malinga ndi mkulu wa gululi a Peterson...
Apolisi ku Mangochi akufunafuna mayi Gladys Lingoni amene wathawa pomuganizira kuti watentha manja a mwana wake wa zaka zisanu ndi chimodzi chifukwa anadya ndiwo za...
Mphunzitsi wa timu yaikulu ya dziko lino ya Flames, Patrick Mabedi, wati timu yake yagonja ndi timu ya Burundi kaamba kakuti siinakonzekere bwino. Mabedi wati...
Anthu ena omwe apindula ndi mtukula pa khomo m’boma la Karonga ati ndondomekoyi yasintha miyoyo yawo pa chuma. Anthuwa anena izi pomwe mlembi ku unduna...
Bungwe loyendesa chisankho m’dziko muno la MEC lalowa mu m’gwirizano obwerekana katundu oyendetsera chisankho ndi bungwe loyendesa chisankho la ECZ la m’dziko la Zambia. Ngati...