Bungwe lolimbikitsa ufulu wa anthu a chialubino la Standing Voice lati ndi zokhumudwitsa kuti anthu ambiri akupitilira kutchula anthuwa maina onyazitsa, zomwe ati ndi kuphwanya...
Mlembi wamkuru wa mpingo wa Zambezi Evangelical a Robert Yanduya ati ndipofunika kuti abusa mu mpingowu akhale zitsanzo zabwino pautumiki wawo ati poti anthu masiku...
Msonkhano waukulu wa chipani cha People’s (PP) wapereka mphamvu kwa atsogoleri omwe asankhidwe kudzachita mgwirizano ndi zipani zina zomwe adzafune kuyenda nazo limodzi pa chisankho...
Apolisi kwa Makawa m’boma la Mangochi agwira Gladys Lingoni azaka 41 powaganizira kuti anatentha manja a mwana wawo wamwamuna wazaka zisanu ndi chimodzi chifukwa chokuti...
Katswiri oyimba nyimbo zauzimu Levysai Kalepa yemwe amakhala ku England koma ndi nzika ya dziko lino wati waganiza zodzatumikira ku Malawi pofuna kupereka mpata kwa...
Bungwe lotolera misonkho la Malawi Revenue Authority MRA lati likukumana ndi mavuto pa ntchito yotolera misonkho, maka pa galimoto zimene zimalowa m’dziko muno mozemba. Mkulu...
Msonkhano waukulu wa chipani cha People’s (PP) wayamba munzinda wa Lilongwe, komwe nthumwi za chipanichi zoposa 1000 zisankhe adindo atsopano. Wapampando wa komiti yomwe yakonza...
Nthumwi 1,100 zochekera mzigawo zonse za dziko lino za chipani cha People’s zikuyembekeza kusankha atsogoleri atsopano a chipanichi pa msonkhano waukulu wa chipanichi, umene uyambe...
Boma la Japan lithandiza dziko la Malawi ndi mpunga wa matani okwana pafupifupi 1900, amene ndi matumba oposa 30,000, kuti agawire anthu amene alibe chakudya...