Mwini watsamba la mchezo la Mikozi, a Bright ‘Excess’ Chiligo, watsutsa mphekesera zimene zikumveka kuti tsamba lake anthu alichita chiwembu kuti lisowe pa makina a...
Wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino, Dr Michael Usi, atsekulira msonkhano waukulu wa chaka chino okambirana njira zolimbikitsa anthu kugwiritsa ntchito magetsi oyendera mphamvu ya...
Apolisi kwa Jenda m’boma la Mzimba akusungira m’chitokosi a Darison Jonazi, 42, amene ndi mwini wake wa shabini ku Embangweni powaganizira kuti anadula zala zakuphazi...
National Bank of Malawi (NBM) yasaina mgwirizano ndi kampani za Sky Energy Africa komanso 265 Energy. Mu mgwirizanowu, makasitomala a NBM adzigula katundu wa kampani...
Atsogoleri a mipingo ku Likuni ndi kwa Chinsapo ku Lilongwe apereka penti yokwana malita 35 ku Polisi ya Chinsapo Unit kuti akonzere denga limene liri...
Chipani cha Malawi Congress (MCP) chati anthu ayenera kulemekeza mzimu wa yemwe anali wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino malemu Dr.Saulos Chilima posauseweretsa pa nkhani...
Meke Mwase amusakha ngati mphunzitsi watimu ya Mighty Mukuru Wanderers kulowa m’malo mwa Nsazurwimo Ramadan yemwe anatula pansi udindowu mwezi wa May. A Ramadan anatula...
Yemwe akufuna kudzayimira chipani cha Malawi Congress (MCP) pampando wa phungu kum’mwera m’boma la Ntcheu, a Joe Ching’ani, ati pakufunika kulimbikitsa maphunziro a sukulu za...
Bungwe la Anti-Corruption Bureau (ACB) lachenjeza matimu khumi ndi awiri amene afika ndime yotsiriza yamu ligi ya Chipiku kuti asamachite katangale pamasewero awo. Chenjezoli likudza...