Anthu omwe amasungitsa ndalama zawo mu banki zosiyasiyana m’dziko muno akhala ndi chitsimikizo chochuluka cha chitetezo pa nthawi yomwe bank zingalephere kupitiriza ntchito. Izi zili...
Akhristu a Mpingo wa Seventh day Apostolic amene amakhala mmapiri akwa Changamtole ndiku Mtazi dera la Mfumu yayikulu Zilakoma ku Nkhatabay awachenjeza kuti ayambe kupita...
Apolisi ku Lilongwe amanga Thokozani Charles wazaka 24 pomuganizira kuti anaba mafoni a mmanja awiri a ndalama pafupifupi K300,000 a mayi wina yemwe anamunamiza kudzera...
Chipani cha Malawi Congress (MCP) chapempha anthu a mdera la Lilongwe Kumachenga kuti akalembetse mwaunyinji mu kaundula wa bungwe la Malawi Electoral Commission (MEC) kuti...
Katakwe otchaya nkhonya, Ellen Simwaka, wati wayika chidwi chofuna kutenga lamba wa World Boxing Council (WBC) akapatsidwa mpata okumana ndi amene akufunanso lambayu. Simwaka wayankhula...
Chipani cha Malawi Congress (MCP) chati sichikhala nawo ku msonkhano waukulu wa chipani cha United Democratic Front (UDF) potsatira mphekesera yoti zipani zina zotsutsa zachita...
Bungwe la Save the Children lati ntchito za maphunziro ndi umoyo wabwino m’sukulu za m’dziko muno zikufunika kuunikidwa ndikukonzedwanso mwakuya komanso mwamakono pofuna kuthana ndi...
Bungwe lomwe limayang’anira ntchito za masewera a mulosera la Malawi Gaming and Lotteries Authority (MAGLA) lati ntchito yolimbikitsa miyambo ya chikhalidwe ikuyenera kuthandiziridwa mokwanira pofuna...
Mawu oti pochoka pamsasa saipitsa ndi amene yagwira bungwe la USAID imene yapereka galimoto zitatu zandalama pafupifupi K380 million ndi katundu wina ku nthambi yoona...