Category : Nkhani
‘Nduna yayikulu ku UK idzigula yokha zovala, magalasi a maso’
Nyumba yowulutsa mawu ya BBC yati nduna yaikulu ya m’dziko la United Kingdom, a Sir Keir Starmer, asiya kulandira thandizo la ndalama zoti adzigulira zovala...
The Harps ikondwerera zaka khumi zamaimbidwe ndi makwaya aku Zimbabwe ndi Zambia
Gulu loimba mingoli yauzimu m’dziko muno la The Harps laitana makwaya aku Zambia ndi Zimbabwe pachikondwerero cha zaka khumi zamaimbidwe pomwenso likukhazikitsa chimbale chatsopano. Makwaya...
MCP ikufuna zipani zidzichita misonkhano mwaufulu
Chipani cha Malawi Congress (MCP) chati ndikofunika kuti chipani chilichonse m’dziko muno chidzilemekeza ufulu wa demokalase komanso kuchita misonkhano mwa mtendere ndi bata. Mlembi wamkulu...
‘Kulimbikitsa ukhondo ndi udindo wa tonse’
Bungwe la IsraAID lapempha ochita malonda mu msika wa Mbayani ku Blantyre kuti adzikhala a ukhondo n’cholinga chakuti apewe kufala kwa matenda monga Cholera. Mkulu...
Bangwe yapha Bullets
Timu ya FCB Nyasa Big Bullets yagonja ndi timu ya Bangwe All Stars 1-0 pa bwalo la masewero la Kamuzu kudzera mu chigoli cha James...
‘Boma likukumana ndi zovuta polimbana ndi mchitidwe wa nkhanza kwa anthu achikulire’
Unduna owona zachisamaliro cha anthu wati ndiokhumudwa kuti anthu achikulire akupitilira kuphedwa ndi kuchitiridwa nkhanza mdziko muno ngakhale kuti malamulo oletsa mchitidwewu alipo. Nduna yaona...
Akakhala ku ndende zaka 19 chifukwa chovulaza mkazi wake wakale
Bwalo lamilandu ku Lilongwe lalamula mwamuna wazaka 51, Ndaona Kabango, kukakhala ku ndende zaka 19 chifukwa chokhapa mkazi wake wazaka 46, Charity Kamumayani, ndi chikwanje...

