Malawi Broadcasting Corporation
Local Local News Nkhani Sports Sports

Wanderers yavomereza Mwase

Meke Mwase amusakha ngati mphunzitsi watimu ya Mighty Mukuru Wanderers kulowa m’malo mwa Nsazurwimo Ramadan yemwe anatula pansi udindowu mwezi wa May.

A Ramadan anatula pansi udindo ngati mphunzitsi kutsatira kusachita bwino kwa timuyi.

Mwase wakhala ali mphunzitsi ogwilizira ku timuyi.

Iye akusankhidwa pamene timuyi ili panambala yachiwiri mu super ligi ndi mapointi 41.

Olemba: Praise Majawa

Related posts

MUST ichititsa chionetsero cha chikhalidwe

Rabson Kondowe

First phase of Israel -Mw labour Export deal kick starts

Alinafe Mlamba

Three men in custody for possession of endangered species

Romeo Umali
error: All Content is protected. Copyright © 2022. Malawi Broadcasting Corporation. All Right Reserved.