Alimi achitsanzo amene ali mu ndondomeko yokhala ndi chakudya chokwanira pakhomo alangiza alimi anzawo m’dziko muno kuti ayike chidwi paulimi wa mtayakhasu. Iwowa ali mu...
Anthu ambiri munzinda wa Blantyre ati ndi okondwa kwambiri kaamba kakuchuluka kwa sugar yemwe akupezeka m’masitolo komanso malo ochitira malonda ambiri. Pakadali pano, mtengo wa...
Mlembi wa mkulu wa chipani cha Malawi Congress (MCP) a Richard Chimwendo Banda walimbikitsa anthu m’boma la Lilongwe kuti adzavotere mtsogoleri wa dziko lino Dr...
Bungwe la National Economic Empowerment Fund (NEEF) lalimbikitsa alimi m’dziko muno kuti adzichitanso ulimi wa ziweto pambali pochita ulimi wa mbewu zosiyanasiyana. Mkulu wa bungweli,...
Prezidenti wakale wadziko lino, Professor Peter Mutharika, wabwerera kuno kumudzi lero masanawa. A Mutharika, omwenso ndi mtsogoleri wachipani chotsutsa cha Democratic Progressive, afika kuno kumudzi...
Phungu wanyumba ya malamulo wadera la Lilongwe City South East, yemwe pano akufuna kudzayimira dera la Lilongwe Mlodza, a Ulemu Msungama, wayamikira mtsogoleri wa dziko...
Bwalo lalikulu lomva milandu yaza chuma ku Blantyre lakana pempho la a Norman Chisale kuti lisinthe mfundo zina pa mlandu umene ukukhudza chuma chimene yemwe...
FDH Bank yalengeza kuti ithandiza ligi yadziko lonse yamasewero ampira wamanja (Netball) ndi ndalama zokwana K1.2 billion kwa zaka zinayi. Kotero, chaka chili chonse bankiyi...
Mmodzi wa ounikira nkhani za utsogoleri wabwino, Undule Mwakasungula, wayamikira mtsogoleri wa dziko lino, Dr Lazarus Chakwera, pobweretsa chikhulupiliro mwa a World Bank pamene yapereka...
Osewera wakale wa timu ya pfuko lino, Flames, Chimango Kayira, wati akukhulupilira kuti masewero apakati pa South Africa ndi Malawi, amene alipo masanawa pa bwalo...