Chipani cha National Youth Alliance (NYA) chati mtsogoleri wa chipani cha Malawi Congress (MCP) yemwenso ndi mtsogoleri wa dziko lino Dr Lazaurus Chakwera ndi yekhayo...
Ntchito yodzipezera malo mu ndime yadziko lonse mumpikisano wa 1 NICO Netball m’chigawo chapakati tsopano yafika pachimake pamene matimu a CIVO Nets ndi Blue Eagles...
A Agness Nkhoma, omwe akuchita ulimi pamodzi ndi amunawo kwa Mkanda m’boma la Mchinji, ati akuyembekezera kupeza ndalama zoposera K650 million kuchokera ku chimanga chomwe...
Ngati gawo limodzi lokumbukira tsiku la mwana wa mu Africa, bungwe la Plan International mogwirizana ndi mabungwe ena, ati ana m’dziko muno akufunika thandizo lalikulu...
Chinthuzi: MANA Mlembi wamkulu wa chipani cha Malawi Congress (MCP), a Richard Chimwendo Banda, ati Prezidenti Dr Lazarus Chakwera ndi chiyembekezo chokhacho cha aMalawi pa...
Mtsogoleri wa dziko lino Dr Lazarus Chakwera yemwenso ndi mtsogoleri wa chipani cha Malawi Congress Party (MCP) akhazikitsa ndondomeko za mfundo za chitukuko zimene chipani...
Anthu a kummwera kwa boma la Ntchisi atsindika kuti voti yawo adzapereka kwa mtsogoleri wa dziko lino, Dr Lazarus Chakwera komanso phungu waderali, a Ulemu...
Bungwe la Malawi Red Cross Society (MRCS) lati lamaliza ntchito yogawa ndalama kwa mabanja amene anakhudzidwa ndi namondwe Judy m’boma la Phalombe m’chaka cha 2023....