Category : Nkhani
Tilambula msewu pakati pa Mwansambo ndi Mponela – Chimwendo Banda
Mlembi wamkulu wa chipani cha Malawi Congress, a Richard Chimwendo Banda, atsimikizira anthu aku Nkhotakota kuti boma lilambula msewu wa pakati pa Mwansambo m’bomalo ndi...
GEFT ichepetsa mavuto obwera ndi kusintha kwa nyengo — Boma, UNDP
Boma, molumikizana ndi bungwe la UNDP, lakhazikitsa ntchito ya gawo lachiwiri komanso lachitatu ya Green Economic Transformation Facility (GETF). Ntchitoyi ikupereka danga kwa anthu komanso...
Ana aphunzitsidwe njira zodzitetezera ku nkhanza zogwiliridwa
Ena mwa akatswiri oona zamalingaliro m’dziko muno ati pakufunika maphunziro ozindikiritsa ana osaposera zaka 13 momwe angadzitetezere kum’chitidwe wankhanza zogonana poyang’anira kukula kwa m’chitidwewu m’dziko...
Zokonzekera gawo lachiwiri lokonza sikimu ya Mlambe zili mchimake
Alimi omwe akuchita nawo ulimi wa mthilira wa minda ikuluikulu pa sikimu ya Mlambe Irrigation ku Mangochi, ayamikira bungwe la Green Belt Authority (GBA) kaamba...
Ntchito za GESD zakondweretsa anthu m’boma la Chiradzulu
Anthu a m’boma la Chiradzulu ati ndi okondwa kamba ka ntchito za chitukuko zosiyanasiyana zomwe zikuchitika kudzera mu thumba la ntchito za chitukuko laboma la...
NEEF yakhazikitsa ngongole ya ulimi wa mthilira
Bungwe la National Economic Empowerment Fund (NEEF) lakhazikitsa ntchito ya ngongole yaza ulimi wa mthilira m’chigawo cha m’mphepete mwa nyanja. Mkulu wabungweli, a Humphrey Mdyetseni,...
Adzudzula mmodzi mwa atsogoleri a DPP kaamba kolankhula moopseza
Bungwe la Civil Society Elections Integrity Forum ladzudzula mmodzi mwa atsogoleri a chipani cha Democratic Progressive (DPP) a Norman Chisale kaamba ka mchitidwe olankhula mau...
MAREP 9 yathandiza anthu aku Dedza
Anthu okhala m’mudzi mwa a Gulupu a Kaname mdera la Mfumu yayikulu Chilikumwendo m’boma la Dedza ati apindula ndi ntchito yolumikiza magetsi m’madera akumudzi ya...

