Category : Nkhani
Alimi asamale pogula mbewu — Self Help Africa
Bungwe la Self Help Africa lalangiza alimi m’boma la Dedza kuti asamale pogula mbewu ndi zipangizo za ulimi mu nyengo ya dzinja chifukwa akagula mbewu...
Galimoto 40 zonyamula mafuta zafika m’dziko muno, zinanso 70 zifika – NOCMA
Pofuna kuonetsesa kuti mafuta a galimoto maaka diesel akupezeka m’malo onse omwetsera mafuta m’dziko muno, bungwe la National Oil Company of Malawi (NOCMA) lati galimoto...
T/A Amidu alowa mmanda
Malemu Mfumu Yaikulu Amidu awayika mmanda lero ku likulu kwa ufumu wawo ku Nangulungutiche ku Balaka. Mfumuyi dzina lawo lenileni linali Amina Gayesi ndipo anamwalira...
Amumanga atapha mkazi wake wamkulu
Apolisi ku Lilongwe amanga Jonas Sainani wazaka 45, pomuganizira kuti wapha mkazi wake wamkulu, Rosemary July wazaka 44. Izi zachitika kunyumba kwa mkazi wake wang’ono....
MWASIP ilimbikitsa kalembera wa malo
Unduna wa zamalo wati wakwanitsa kulembera malo oposa 50,000 mukaundula wamalo a umwinimwini, pansi pa ntchito ya chitukuko cha Malawi Watershed Services Improvement Project (MWASIP)...
Mashehe adandaula chifukwa mabanja sakulimba
Mkulu wa ma Sheikh m’dziko muno, Grand Mufti Muhammad Uthman, wadandaula ndi mchitidwe othetsa mabanja m’dziko muno, ngakhalenso a chipembedzo cha chisilamu. A Uthman anati,...
Msewu wa Nkhotakota tiumaliza komanso ukhala wapamwamba – Chakwera
Prezidenti wa dziko lino, Dr Lazarus Chakwera, ali m’boma la Nkhotakota kumene, mwazina, akuona ntchito zachitukuko cha msewu wa M5 omwe boma la Malawi likumanga...

