Mmodzi kwa akuluakulu oona za maphunziro msukulu za m’madera akumidzi m’boma la Blantyre, a Alfred Mphandamkoko, wati malo ophunzira abwino komanso zipangizo zokwanira ndizofunika pokopa...
Mlimi wa ku Blantyre, a Mariko Kalima, wayiphula pamene wapata K2.5 million mu mpikisano wa Tisanje umene ikupangitsa ndi kampani yopanga sopo ya Hirwa General...
Queens yagonja 65-35 ndi South Africa mu mpikisano wa m’mayiko a mu Africa umene ukuchitikira m’dziko la Namibia. Malawi, yomwe inagonjetsa Zambia mu masewero ake...
Wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino, Dr Michael Usi, watsindika kufunika kwa mgwirizano wabwino pakati pa atsogoleri amabungwe omenyera ufulu wa anthu komanso boma pa...
Apolisi munzinda wa Zomba amanga a Jessie Mpanira, 35, powaganizira kuti amafuna kulowetsa chamba ku ndende ya Zomba Maximum. Wachiwiri kwa ofalitsa nkhani za polisi...
Nyumba youlutsa mawu ya boma, Malawi Broadcasting Corporation (MBC), yasayina mgwirizano ndi bungwe la Water Aid. Cholinga cha mgwirizanowu ndi kupititsa patsogolo nkhani zokhudza ukhondo...
Mlembi wamkulu mu unduna oona zokuti pasamakhale kusiyana pakati pa amuna ndi akazi ndi zosamalira anthu, Dr. Nertha Semphere Mgala, wati boma kudzera mu undunawu...
M’busa Clifford Kawinga, amene ndi mtsogoleri wa mpingo wa Salvation for All Ministries, walimbikitsa mafumu m’boma la Mchinji kuti adzikhulupilira komanso kupempha nzeru kwa Mulungu,...