Wachiwiri kwa mtsogoleri wadziko lino, Dr Michael Usi, wachenjeza kuti boma sililekelera mchitidwe wachinyengo pakati pa akuluakulu amene akugwira ntchito yopereka chakudya ku mabanja omwe...
Ophunzira pa sukulu yaukachenjede ya University of Malawi(Unima) ku Zomba akhazikitsa chipangizo chothandiza anthu omwe ali ndi ulumali wosaona. Mmodzi mwa ophunzirawo, Hudson Mwangalika, wati...
South West Police Region has commended the business community in the region for supporting them in strengthening security ahead of the festive season. Commissioner of...
Anthu opyola 8,000 m’ma boma a Mulanje ndi Phalombe tsopano ali ndi madzi aukhondo kutsatira chitukuko chimene nthambi ya DoDMA yachita m’madera a Kamwendo ndi...
Achinyamata a mdela la Mfumu yaikulu Mwirang’ombe ku Wovwe m’boma la Karonga awayamikira chifukwa chokhala ndi chidwi kuti aphunzire ntchito zaluso la manja mdelari. Mfumu...
Nthambi yoona za nyengo yati namondwe Chido tsopano wabwelera m’dziko la Mozambique atachepa mphamvu. Mkulu oona za nyengo ku nthambiyi, a Lucy Mtilatila, ati namondweyu...
Ogwira ntchito zofalitsankhani ku nthambi ya apolisi m’dziko muno awalimbikitsa kuti aike chidwi chachikulu pothandizira ntchito yoteteza amayi ku mchitidwe wa nkhanza mu nthawi ya...
Anthu a midzi ya Mphampha ndi Tsambalabooka kwa mfumu yaikulu Lundu ku Chikwawa ati ndi okondwa kuti tsopano adzimwa madzi aukhondo. Anthuwa anena izi kampani...
Bungwe loona za madzi la Southern Region Water Board (SWRB) lati ntchito yomanga malo omwe adzipereka madzi kwa anthu okhala mmadera ozungulira Makanjira ku Mangochi...