Category : Nkhani
TIGWIRANE MANJA NDI BOMA PA CHITUKUKO -MATOLA
Nduna yoona zamphamvu zamagetsi a Ibrahim Matola yati nkofunika kuti anthu onse m’dziko muno agwirane manja popititsa patsogolo chitukuko mogwirizana ndi masomphenya a mtsogoleri wa...
OYIMBA OMWE ANALI PANSI PA NDE’FEYO AIMBA LERO KU BLANTYRE
Zokonzekera zonse za phwando la mayimbidwe limene likutchedwa kuti Nde’feyo legacy, lomwe lichitikire ku 24/7 ku Blantyre lero, zili mchimake. Mwambowu ubweretsa pamodzi oyimba asanu...
ZAMBIRI MWA ZIMENE A CHAKWERA ANALONJEZA MU SONA YA 2023 ZACHITIKA – NDUNA
Nduna zosiyanasiyana zati zambiri mwa zomwe mtsogoleri wa dziko lino, Dr. Lazarus Chakwera, analonjeza kuti zichitike mu uthenga wawo wa SONA chaka chatha, zakwaniritsidwa. Mwachitsanzo,...
MAKHANSALA AWIRI A DPP ALOWA MCP KU PHALOMBE
Makhansala awiri a chipani cha Democratic Progressive (DPP) atuluka mchipanichi ndipo alowa cha Malawi Congress (MCP). Mkulu okopa anthu mu MCP a Moses Kunkuyu alandila makhansala...
BOMA LAPEZA MISIKA YAMBIRI YAMBEWU ZA ALIMI
Boma latsimikizila alimi mdziko muno kuti asade nkhawa za misika komwe akagulitse mbewu zao. Nduna ya zaulimi a Sam Kawale anena izi atayendela alimi omwe...
UNDUNA WAZA CHUMA UKULINGALILA ZOONJEZELA NDALAMA KUBUNGWE LA NEEF
Nduna ya zachuma a Simplex Chithyola Banda ati unduna wao uonetsetsa kuti wapereka ndalama zokwanila ku bungwe la NEEF. Poyankhula pomwe akuyendela ntchito za NEEF ...

