President Lazarus Chakwera wati khalidwe lonyoza anthu achikulire powanena kuti ndi mfiti ndi kuwapha (mob justice) zili ndi kuthekera kosokoneza ana achichepere m’dziko muno.
A Chakwera ati ndi pofunikanso kukhala ogwirizana, posatengera kusiyana zipani, zipembedzo ndi zina zambiri popeza anthu akakhala ogwirizana, dziko lino likhoza kupambana nkhondo yolimbana ndi njala.
#ChakweraDevelopmentalRally