Prezidenti Dr Lazarus Chakwera wauza anthu amchigawo chakumpoto kuti boma lake ladzipereka potukula miyoyo ya anthu mdziko muno kudzanso mchigawochi. Dr Chakwera amalankhula pa Katoto...
Mai wa fuko lino, Madam Monica Chakwera, lero akutsogolera amayi m’dziko muno pa mwambo wa tsiku la mapemphero a amayi pa dziko lonse. Mwambowu ukuchitikira...
Chinthuzi: Tsamba la mchezo Unduna wa maboma ang’ono wauza khonsolo ya mzinda wa Lilongwe (LCC) kuti ileke ntchito yotchetcha chimanga mminda ya anthu ena mumzindawu...
Komiti yoona za chitetezo komanso ubale wa dziko lino ndi maiko ena yabweza ena mwa akuluakulu a nthambi yoona zolowa ndi kutuluka m’dziko muno kaamba...
Banki yayikulu padziko lonse ya World Bank yati ndondomeko yazachuma ya dziko la Malawi yachaka cha 2024/2025 yomwe yaperekedwa sabata yatha, ikupereka chiyembekezo kuti chuma...
Mkulu oyang’anira ndende za m’dziko muno, a Masauko Ng’ombeyagwada Wisikoti, ati kundende ndi malo othandiza kusintha khalidwe la munthu osati malo ongokhaulitsira iwo ophwanya malamulo....
M’buyomu: Ma Bishop a mpingo wakatolika ndi mtsogoleri wa dziko lino, Dr Lazarus Chakwera. Boma lati lipitiriza kuyankhulana komanso kumvana ndi ma Bishop a mpingo...
Mmodzi mwa anthu amene amayankhulapo pa nkhani zosiyanasiyana, maka zolimbikitsa ulamuliro wabwino, a Undule Mwakasungula, ati dongosolo la zachuma lomwe alipereka mnyumba ya malamulo lachisanu...