Kampani ya Electricity Supply Corporation of Malawi (ESCOM) yati $21 million yomwe mtsogoleri wa dziko lino Dr Lazarus Chalwera anakatenga ku msonkhano wa COP27 ithandizira...
Timu ya Silver Strikers, yomwe ikuteteza ukatswiri waligi ya TNM, yagonja 1-0 ndi FCB Nyasa Big Bullets pamasewero amene anali pa bwalo lamasewero la Bingu...
Malawi yagonja 2-0 ndi Tunisia pa bwalo la masewero la Stade Olympique Hammadi Agebri munzinda wa Tunis. Awa anali masewero a mpira wamiyendo odzigulira malo...
Bungwe la Strengthening Science and Mathematics Education in Africa (SMASE) lati dziko la Malawi lili ndi kuthekera kokhala mphika waza ulimi mu Africa pokhapokha patakhala...
Mabungwe amene si aboma ayamikira boma poyika thumba lapadera la K1 bilion lothandiza ntchito za mabungwewa. Mkulu wa bungwe la Non-Governmental Organisation Regulatory Authority (NGORA),...
Wachiwiri kwa nduna ya za umoyo, a Noah Chimpeni, atsindika kuti dziko la Malawi liri ndikuthekera koyendetsa ntchito za umoyo popanda thandizo la dziko la...
Oyendetsa ndi kukonza Ku Mingoli Bash, a Sound Addicts Live, ati mwambowu udzachitika m’chaka cha 2026 m’malo mwa chaka chino ku Cape Maclear m’boma la...
Mtsogoleri wakale wa bungwe la Film Association of Malawi (FAMA), a Gift Sukali, wafunira zabwino atsogoleri atsopano amene bungweli lawasankha kumene. A Sukali ati ndi...