Nsanje District Officials have expressed satisfaction with the progress of the Bangula-Marka railway construction works. On Tuesday, the District’s Commissioner, Dominic Mwandira, said there is
People from the area of Traditional Authority Nkaya in Balaka have applauded Balaka District Council for the construction of a K93 million health post, which
Apolisi m’chigawo chakummwera amanga Richard Herema wazaka 42, yemwe kwawo ndi ku Mozambique, pomuganizira kuti iyeyo pamodzi ndi amzake,l anathyola nyumba ziwiri ndikuba ndalama zoposa
Apolisi mu mzinda wa Zomba amanga a Andrew Banda a zaka 25 zakubadwa powaganizira kuti anagwirira mwana wazaka 12. Ofalitsankhani wa Polisi ya Zomba, a
Malawi Broadcasting Corporation (MBC) and the Media Institute of Southern Africa (MISA) Malawi Chapter have extended their condolences to the family of the late Geoffrey
Khothi la Magistrate mu mzinda wa Blantyre la lamula kuti abambo atatu akagwire ukayidi kwa zaka ziwiri komanso chaka ndi theka kaamba kopezeka olakwa pochita
Bwalo la Milandu la High Court mumzinda wa Lilongwe lathetseratu mlandu wa pakati pa ochita malonda a ku Nsungwi, Area 25 ndi m’mwenye Akbar Salahudding
Nduna yoona za madzi komanso ukhondo, mayi Abida Mia, pamodzi ndi anthu ena ambiri, asonkhana ku Machinjiri Area 3 mu mzinda wa Blantyre kumene akukhuza