Khwimbi la anthu likukhamukira ku bwalo la zamasewero la Mulanje kumene kukhale mwambo wokumbukira kuti patha chaka chimodzi chichitikireni Namondwe wa Freddy.
Prezidenti wa dziko lino, Dr Lazarus Chakwera, ndiye atsogolere nwambowu komwe kwafika kale anthu osiyanasiyana, kuphatikizapo mafumundi akuluakulu ena.
Olemba : Blessings Cheleuka