Bungwe la Malawi Union of Savings and Credit Cooperatives (MUSCCO) lapempha alimi m’dziko muno kuti asagulitse mbewu zawo kwa ochita malonda osatsata ndondomeko ndi cholinga...
Mtsogoleri wa dziko lino Dr Lazarus Chakwera wati ndi kofunika kuti chitetezo chikhale chokhwima pofuna kuthana ndi atambwali amene amazembetsa fodya kupita naye ku maiko...
A Eisenhower Mkaka omwe ndi mlembi wamkulu wa chipani cha MCP ayamikila m’tsogoleri wa dziko lino Dr Lazarus Chakwera kaamba kopititsa patsogolo ndale za demokalase....
Alimi ang’ono ang’ono olima mpunga omwe amagwilira ntchito mmagulu kwa Maganga m’boma la Salima akuyembekezera kupha makwacha ndi ulimi wamakono wa mpunga kutsatira kuchita bwino...
Bungwe lotchedwa We Effect, lomwe limagwira ntchito ndi alimi ang’ono ang’ono omwe ali m’magulu, lalimbikitsa alimiwa kuchita malonda ena apadera posadalira ulimi okha pofuna kupeza...
Mtsogoleri wa dziko lino, Dr Lazarus Chakwera, wanyamuka m’chigawo chakummwera, kudzera pa bwalo la ndege la Chileka, kubwelera ku Lilongwe. A Chakwera anali m’chigawo chakummwera...
Wachiwiri kwa Chancellor wa sukulu ya ukachenjede ya Malawi University of Science and Technology (MUST), Professor Address Malata, wati atsikana onse omwe anawasankhira ku sukuluyi...