Banki ya NBS yakhazikitsa mpikisano watsopano wa alimi omwe akuutcha K14 million yonyotsolerana, momwe alimi komanso makasitomala abankiyi adzipata mphotho zosiyanasiyana popikisana kusunga ndalama. Poyankhula...
Nduna yazamalo a Deus Gumba atsindika kufunika kogwira ntchito limodzi ndi apolisi pantchito yolimbana ndi kuthetsa mikangano yokhudza malo m’dziko muno. Ndunayi yanena izi ku...
Prezidenti wa dziko lino, Dr Lazarus Chakwera, wati ndi wokonzeka kudzaimira chipani cha Malawi Congress MCP ngati msonkhano waukulu wachipani umene ukhalepo mmwezi wa August...
Anthu ochuluka akhamukira pabwalo la Mzonde kwa mfumu yaikulu Kalolo ku Lilongwe komwe mtsogoleri wadziko lino, Dr Lazarus Chakwera, pamodzi ndi mkulu wa Millennium Challenge...
Bungwe la MACRA la limbikitsa a Malawi kuti adzikamang’ala ku Polisi ngati anthu ena awalakwira kapena kuwachitira upandu pa masamba a mchezo komanso malo ena...
Gulu la mabungwe omwe si aboma m’dziko muno la Citizen Alliance layamikira boma pa zomwe likuchita pobwezera m’chimake chuma cha dziko lino. Muchikalata chomwe achiwerenga...
Sipikala wanyumba yamalamulo a Catherine Gotani Hara ati dziko lino litengerepo mwayi paubale omwe ulinawo ndi dziko la China popititsa patsogolo ntchito zamalonda. A Hara...
Boma la United States, kudzera ku bungwe la USAID, lapereka K12 billion ku boma la Malawi kuti zithandizire anthu amene akhudzidwa ndi njala. Polengeza za...