Phungu wa Dera la Nsanje Lalanje, wayamikira boma pobweretsa chitukuko cha nyumba ya ma kompyuta pa sukulu ya Phokela CDSS mderalo. Phunguyi, a Gladys Ganda,...
Timu ya Silver Strikers idakali patsogolo pa m’ndandanda wa matimu amu TNM Super League itagonjetsa timu ya FCB Nyasa Big Bullets 1-0 Lamulungu pa bwalo...
Mulhoko wamphirameto wa FCB Nyasa Big Bullets wookelhemulhiwa ni Silver Strikers vamatheelha ayo yeereyelha va Kamuzu Stadium o Blantyre. Chinsisi Maonga amulhoko wa Silver Strikers...
Wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino Dr Saulos Chilima tsopano wafika m’dziko la Republic of Korea kumene akachite nawo msonkhano waukulu pakati pa dzikolo ndi...
Masana ano matimu a FCB Nyasa Big Bullets ndi Silver Strikers akhala akuthambitsana pa bwalo la Kamuzu mu mzinda wa Blantyre. Chochititsa chidwi ndi chakuti...
Kuvumba mabindula madzulo ano pa Kamuzu Institute of Sports pakati pa ziphona zazigogodo ziwiri Limbani Masamba komanso Simeon Tcheta pa nkhonya yolimbirana lamba yomwe yakonzedwa...
Bungwe la National Economic Empowerment Fund (NEEF) latsimikiza kuti lipitiriza ntchito yothandiza anthu, kuphatikizapo amene anakhudzidwa ndi kusefukira kwa madzi m’dziko muno. Wapampando wa bungweli,...
Inenelhi dha Mighty Mukuru Wanderers dhohaatuthilha omulhihani athokothoko amulhoko wa Premier Bet Dedza Dynamos vamatheelha ayo yeereya va Kamuzu Stadium o Blantyre. Chistopher Kumwembe sika...