Kazembe oyimila dziko la Malawi ku Vatican a Joseph Mpinganjira ati kukumana kwa prezidenti Dr Lazarus Chakwera ndi mtsogoleri wa mpingo wa akatolika pa dziko...
Chipani cha UTM chalimbikitsa achinyamata kuti alembetse mu kaundula wa unzika kuti adzakhale ndi mwai oponya nawo voti pachisankho chachikulu chomwe chichitike mdziko muno chaka...
M’busa wa mpingo wa Lilongwe CCAP, umene uli pansi pa Synod ya Livingstonia, a Nase Chunga, alangiza anthu amene ali paubwenzi ngakhalenso pabanja kuti ngati...
Boma lati mankhwala ophera tizilombo a chroline alibe vuto lirilonse pa umoyo ngakhalenso nkhani zokhudza ubereki. Wachiwiri kwanduna yoona za madzi ndi ukhondo a Liana...
Unduna wa zamaphunziro mogwirizana ndi bungwe loona za mayeso la Malawi National Examinations Board (MANEB) ati mwa ophunzira a sitandade 8 okwana 252, 448 omwe...
Mwamuna wazaka 42, Isaac Patisi, wakadzipereka ku polisi ya Area 3 ku Lilongwe atapha mkazi wake Azefa Kasamanda wazaka 36 pomukhapa ndi nkhwangwa. Mneneri wapolisi...
Mneneri wa chipani cha MCP, a Jessie Kabwila, wati dziko la Malawi likusintha kwambiri pa chitukuko. Poyankhula pamsonkhano wa atolankhani ku Lilongwe komwe akufotokoza za...
Bungwe la Malawi Communications Regulatory Authority (MACRA) lati likufuna mitengo ya ma ‘smartphone’ kapena kuti lamya zammanja zomwe ziri ndi ‘internet’ zikhale zotsika mtengo mdziko...
Akuluakulu a ofesi ya zaumoyo ku khonsolo ya boma la Balaka awayamikira polimbikitsa ntchito yoonetsetsa kuti anthu akulandila thandizo la zachipatala mosavuta. Nduna ya za...