Mafumu a m’maboma a Mzimba ndi Kasungu asayinira mgwirizano ndi akuluakulu a kampani ya Globe Metals and Mining womwe uthandize kuti anthu a mmadera ozungulira...
Akuluakulu a malo ogona alendo a Mount Soche munzinda wa Blantyre ati akwanitsa kuzimitsa moto umene unabuka pamalowo. Malinga ndi mmodzi mwa akuluakuluwo, motowo unabuka...
Alimi a ng’ombe za mkaka m’chigawo cha ku m’mwera apempha madalaivala agalimoto zikuluzikulu kuti asiye kunyanyala ntchito chifukwa akutaya mkaka wambiri. Dzulo lokha, alimiwa ati...
Nduna yowona za chisamaliro cha anthu a Jean Sendeza yalangiza ogwira ntchito zolemba mayina anthu opindula ndi ndalama za Mtukula Pakhomo mdziko muno kuti aganizire...
Wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino Dr Michael Usi ali nawo pa zochitika zokhazikitsa bungwe la Malawi Church and Community Transformation Movement m’chigawo cha kum’mwera....
Mabungwe omwe siaboma ayamba msonkhano wao wamasiku awiri mu mzinda wa Harare mdziko la Zimbabwe omwe ukuunika mwadongosolo zomwe maiko a m’bungwe la SADC anagwirizana...
Pamene anthu a m’boma la Ntchisi akulandira ndalama za Mtukula Pakhomo, banja la a Mvula lalangiza anthu kuti azigwiritse ntchito mwanzeru monga kuchita malonda ang’ono...
Gawo loyamba la ntchito yomanga chipatala cha makono ku Mponela m’boma la Dowa yatsala pang’ono kutha pomwe pali chiyembekezo kuti anthu adzayamba kulandira thandizo pofika...
Mtsogoleri wa bungwe loyang’anira sukulu zomwe sizaboma mdziko muno la Independent Schools Association of Malawi (ISAMA) a Wycliff Chimwendo ati ntchito yauphunzitsi ndi maitanidwe ndipo...