Ena mwa atsogoleri amipingo m’dziko muno ati mtsogoleri wa dziko lino Dr Lazarus Chakwera waonetsa kusakondera kwake posankha anthu atsopano m’ma board a kampani za...
Wachiwiri kwa nduna yaza ulimi Benedicto Chambo anacheza ndi akuluakulu achipembezo chachi Rasta munzinda wa Lilongwe. A Chambo, omwenso ndi phungu wadera la Mangochi –...
Mtsogoleri wa zokambirana mu nyumba ya malamulo, a Richard Chimwendo Banda, wayamika mtsogoleri wa dziko lino Dr Lazarus Chakwera chifukwa chokhala ndi chikhulupiliro mwa amayi...
Akatswiri pa nkhani zamalamulo a Justin Dzonzi ndi a Allan Ntata ati ntchito ikadalipo kwa amene akutsogolera chipani cha UTM, a Dalitso Kabambe, pa nkhani...
Bungwe la Greenbelt Initiative Authority lapereka ntchito ya gawo lachiwiri lomanga malo a mthilira a Nthola-Ilola m’boma la Karonga kwa amene agwire ntchitoyi, a Kabiki...
Bungwe la Transporters Association of Malawi lati kukonza msewu wa Mangochi-Makanjira kudzathandizanso kwambiri kulimbikitsa ntchito za mtengatenga ndi malonda pakati pa dziko lino ndi la...
Mlembi wamkulu wa chipani cha Malawi Congress (MCP), yemwenso ndi nduna ya maboma ang’ono, umodzi ndi chikhalidwe, a Richard Chimwendo Banda, ndiye wanena izi ndikulimbikitsa...
Timu ya Silver Strikers, yomwe ikuteteza ukatswiri waligi ya TNM, yagonja 1-0 ndi FCB Nyasa Big Bullets pamasewero amene anali pa bwalo lamasewero la Bingu...
Bungwe la Greenbelt Authority lati ndi lokhutitsidwa ndi kuchulukwa kwa chimanga chomwe bungweli lalima ku imodzi mwa ma Mega Farm ya Chikwawa Irrigation Scheme m’boma...